Bwalo la milandu ku Chiradzulu lagamula a Matias Kabango a zaka 40 kukakhala kundende kwa zaka 12 chifukwa chogwilira mwana wa dzaka 16. Mneneri wa a polisi ku Chiradzulu a Cosmas Kagulo anati oimila boma pa mulanduwu a Spenard Chankoma anauza bwaloli kuti pa 12 Ogasiti chaka chino a Kabango anamugwilira mwanayu pamene anali kumunda […]
The post Bambo wa zaka 40 amugamula kukhala ku ndede zaka 12 pa mulandu wogwilirira appeared first on Malawi 24.