Bambo wa zaka 32 wafa atagundidwa ndi sitima ku Machinga

Bambo wa zaka 32 yemwe dzina lake ndi Ashan Khalima wafa atagundidwa ndi sitima yapamtunda ku Machinga. Mkulu wa a Police Boma la Machinga Senior Assistant Commissioner Jane Mandala watsimikidza zangoziyi poyankhula ndi Malawi24. A Mandala ati ngoziyi idachitikira mdera lotchedwa Mphonde cha m’ma 10 koloko usiku pafupifupi makilomita 14 kuchokera ku Nayuchi Railway Station. […]

The post Bambo wa zaka 32 wafa atagundidwa ndi sitima ku Machinga appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください