A Phillip Mwanza a zaka 24 awamanga kwa Jenda ku Mzimba powaganizira kuti apha mwana wa mlongo wawo, a Steven Shaba, a zaka 21, ndewu itabuka kamba ka suti yovala pa ukwati Mneneri wa Polisi ya Jenda a Macfarlane Mseteka ati izi zachitika dzulo ku Vibangalala m’bomali. A Mseteka ati a Mwanza anapsa mtima kamba […]
The post Bambo wa zaka 24 wamangidwa chifukwa chokupha mwana wa mlongo wake appeared first on Malawi 24.