Bambo owotcha makala wafa ndi mpweya oyipa

Ku Mangochi bambo wa zaka 32 wamwalira atapuma mpweya oyipa ochokera mu utsi pamene amaotcha makala m’nkhalango ina. Watsimikiza za nkhaniyi ndi ofalitsa nkhani pa polisi ya Mangochi, Amina Tepani Daudi omwe azindikira mzobamboyu ngati a Salabadika Kauma. A Tepani Daudi ati ngoziyi yachitika lamulungu pa 22 October 2023, m’nkhalango ya Namizimu yomwe ili m’dera […]

The post Bambo owotcha makala wafa ndi mpweya oyipa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください