Bambo anyongedwa chifukwa chopezeka ndi mankhwala ozunguza ubongo mdziko la Singapore

Wolemba: Gracious Zinazi Bambo wa zaka 34 wanyongedwa lero lachitatu m’dziko la Singapore chifukwa chopezeka ndi mankhwala ozunguza ubongo a heroin okwana ma sipuni atatu mu chaka cha 2009. Bamboyu ndi Nagaenthran Dharmalingam, yemwe kwawo kwenikweni ndi ku Malaysia. Mayi ake komanso omuimirira pa mulandu anayesetsa kuti amupulumutse potenga ziletso komanso kufotokoza kuti ma lipoti […]

The post Bambo anyongedwa chifukwa chopezeka ndi mankhwala ozunguza ubongo mdziko la Singapore appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です