Bambo amulamula kukakhala ku ndende zaka 11 chifukwa chogwilirira mwana

Bwalo la milandu ku Liwonde mu boma la Machinga lalamula bambo wina wa zaka 27 zakubadwa kuti akakhale ku ndende ndikukagwila ukaidi wakalavula gaga kwa zaka 11 chifukwa chopezeka olakwa pamulandu ogwirilira mwana wa zaka 14. Mkulu wa a Police Boma la Machinga Deputy Commissioner Jane Mandala watsimikiza zankhaniyi poyankhula ndi Malawi24. Deputy Commissioner Mandala […]

The post Bambo amulamula kukakhala ku ndende zaka 11 chifukwa chogwilirira mwana appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください