Mkulu wina wa zaka 35 zakubadwa ku Lilongwe walamulidwa kukakhala ku ndende ndikukagwila ntchito ya kalavula gaga kwa zaka 21 kamba kopezeka olakwa pa mlandu wogwililira mwana wa zaka khumi. Malingana ndi mneneri wa apolisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu, nkhani yonse ikuti mkuluyu yemwe dzina lake ndi Zakaliya Potifala adapempha mwanayo kuti akawatungire madzi […]
The post Bambo amulamula kukakhala ku ndende kwa zaka 21 kamba kogwililira mwana appeared first on Malawi 24.