Bambo wina ku wa zaka 24 wamangidwa ku Kasungu kamba koguna kugulitsa mwana wake pa mtengo wa K7 miliyoni. Bamboyu yemwe dzina lake ndi Noel Kanyama amafuna kugulitsa mwana wake kwa mkulu wina ochita malonda mtauni ya Kasungu. Mneneri wa apolisi ku Kasungu a Joseph Kachikho wati anayimbira foni wa malondayo kuti ali ndi mwana […]
The post Bambo amafuna kugulitsa mwana pa mtengo wa K7 miliyoni appeared first on Malawi 24.