Atha kuona ma demo angati a Jane Ansah naye Masautso Chamkakala chifukwa a mabungwe ndiye akwiya naye. Ati sakuona phindu lake. Mabungwe omwe si aboma ati a Chamkala omwe ndi mkulu wa ofesi ya yoyang’anira zozenga milandu m’dziko muno, Director of Prosecutions (DPP), akuyenera kutula pansi udindo polephera kugwira ntchito yake moyenera. Izi zanenedwa pa […]
The post Azipita Chamkakala – a mabungwe appeared first on Malawi 24.