Pamene madera amchigawo chapakati komanso kumwera kwa dziko lino kuli nga’mba, tsopano nthambi yoona za nyengo ndi kusintha kwa nyengo yati kuyambira lachitatu pa 13 December, a Malawi ayembekezere kulandira mvula ya mphamvu. Malingana ndi chikalata chomwe nthambiyi yatulutsa kudzera mwa m’neneri wa nthambiyi a Yobu Kachiwanda ati mvula ikuyembekezereka kugwa mmadera ochuluka mdziko lino. […]
The post Azanyengo ati kugwa mvula ya mphamvu kuyambira lachitatu likudzali appeared first on Malawi 24.