Anthu ochuluka m’dziko muno akupitilira kukanitsitsa mwantuu wagalu lamulo lomwe walamura posachedwapa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti nyimbo ya fuko iziyimbidwa ndime zonse zitatu. Lachisanu lapitali a Chakwera analamura kuti nthawi zonse pa malo aliwonse amene nyimboyi idziyimbidwa, anthu adziyimba ndime zonse zitatu osangoti ndime imodzi monga momwe anthu akhala akupangira kumbuyo […]
The post Ayimba okha apule, a Malawi amenyetsa nkhwangwa pamwala appeared first on Malawi 24.