Ayi chonde pitani khomo la mtima wanga ndatseka- Watero Jetu

Iyi ndi chorus ya nyimbo ya  oyimba otchuka otchedwa Jetu yomwe wangotulutsa kumene  maola ochepa apitawa. Nyimboyi yomwe dzina lake ndi chakwaza, ikuonetsa kuti mzimayiyu anali ndi chibwenzi dzina lake John ndipo chinatha mosakhala bwino zomwe zinapangitsa kuti asweke mtima. ” Kale unandiuza suli ready za chikondi sizingatheke m’malo mwake mzanga  analowa fisi,” ikutero mbali […]

The post Ayi chonde pitani khomo la mtima wanga ndatseka- Watero Jetu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください