M’modzi mwa madokotala azitsamba odziwika bwino mdziko muno, mai Bwanali am’boma la Neno omwe amadziwika ndi dzina loti Ayaya amwalira. Malingana ndi khansala wa dera la Lisungwi m’boma la Neno a Mark Ngwangwa, mai Bwanali amwalira lachiwiri masana pomwe akuti amadwala nthenda ya kupweteka kwa nsana. Malipoti akusonyeza kuti thupi la malemu Ayaya lilowa m’manda […]
The post Ayaya amwalira atadwala nsana appeared first on Malawi24.