‘Awa ndionama basi’: Makawa wang’alura asing’anga

Lolemba sabata ino, ‘Mbuyache Makawa’ monga momwe amadzitchulira munyimbo zake, watulutsa nyimbo ya tsopano yomwe akuitchula kuti ‘Bosh’ yomwe wajambula ndi Drue G pomwe kanema yake  yajambulidwa ndi Mega. Mu nyimbo ya ‘Bosh’ yomwe tanthauzo lake ndi ‘Bodza’, Makawa akudzudzu makhalidwe omwe a sing’anga akuchita pomabera anthu ndalama pomawanamiza kuti ali ndi mtera osiyanasiyana. Mu […]

The post ‘Awa ndionama basi’: Makawa wang’alura asing’anga appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください