Sukulu ya ukachenjede yomwe ili m’boma la Thyolo ya Malawi University of Science and Technology (MUST) kudzera kwa wachiwiri kwa Chancellor professor Address Malata, ati atsikana onse amene anawasankhila ku sukuluyi ndipo analephera kukayamba chifukwa choti anasowa ndalama zolipilira maphunziro tsopano apite ku sukulu popeza ndalama zapezeka. A Malata ati kampani yopanga suga mdziko muno […]
The post Atsikana osowa fizi ku MUST apulumuka appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
