Bungwe la Media Council of Malawi (MCM) lati likulandira madandaulo ochuluka pa nkhani yakusavala moyenera kwa ogwira ntchito zofalitsa nkhani mdziko muno. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe bungwe la MCM latulutsa lero lolemba pa 3 August, 2023 chomwe asayinira ndi a Moses Kaufa komaso a Wisdom Nelson Chimgwede omwe ndi ena mwa akuluakulu a […]
The post Atolankhani adandaulidwa pakusavala bwino appeared first on Malawi24.
Moni Malawi 