Atoht Manje wamwalira atamaliza kuimba

Thambo lakuda lakuta dziko la Malawi pomwe lataya m’modzi mwa akatswiri oyimba nyimbo za lokolo Elias Misi, yemwe amadziwika ndi dzina loti Atoht Manje. Malingana ndi zomwe tsamba lino lapeza, Atoht Manje wamwalira m’bandakucha wa Lamulungu ku sukulu yaukachenjede ya Livingstonia munzinda wa Mzuzu komwe kunali phwando la mayimbidwe. Mphekesera zikuveka kuti atamaliza kuimba ku […]

The post Atoht Manje wamwalira atamaliza kuimba appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください