Atipweteka, atisenda ndipo atiyalutsa: Ijipiti ya Mo Salah 4 Malawi ya Marinica 0

Zoti tiri pa chisoni sizinaoneke. Zoti tate wathu ndi m’busa sizinaonekenso. Pena kumati mwina malaya ofiyira tinavala lero anamusokoneza mmaso Mo Salah kuti amayesa ndi Manchester United. Chifukwa atiswa ndipo atisambitsa chokweza. Olo naye kochi Mario Marinica wayenda wa uyo uyo pochoka pa Bingu. Zamanyazi zenizeni. Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino lero […]

The post Atipweteka, atisenda ndipo atiyalutsa: Ijipiti ya Mo Salah 4 Malawi ya Marinica 0 appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください