Ati n’kutheka kuti kukondwa kwanu ndi nyimbo ya Chakwaza kukubwera chabe chifukwa mumakonda kuzunza nkhalamba, atero amuna a pa Podcast Malawi. Mkozi wa nyimbo Dumisani Moyo yemwe amatchuka kwambiri ndi dzina loti Blage, ndi m’modzi mwa anthu omwe akuona kuti mwa Jetu mulibe tsogolo pa nkhani ya mayimbidwe ngakhale kuti pano gogoyu watekesa pa Malawi […]
The post Ati Jetu akuzunzidwa – atero a Podcast Malawi appeared first on Malawi 24.