Asilikali awiri omwe anasowa dzulo apezeka

Asilikali omwe anasowa dzulo ku Mulanje pamene boti lomwe anakwera linakokoloka ndi madzi apezeka. Nduna yowona za Chitetezo a Harry Mkandawire ati awiriwa agona mu mtengo ndipo anthu omwe ali kumeneko atsimikiza kuti ayankhulana nao. Malingana ndi nduna ya za ma boma a Richard Chimwendo Banda omwe anali pa Mkando m’boma la Mulanje, dzulo asilikali […]

The post Asilikali awiri omwe anasowa dzulo apezeka appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください