Asilikali apulumutsa nawo anthu ku Dwangwa

Asilikali a dziko lino atenga nawo gawo populumutsa anthu pafupipafupi 200 omwe akhudzidwa ndi madzi osefukira ku Dwangwa m’boma la Nkhotakota. Malingana ndi lipoti lochokera ku khonsolo la Nkhotakota, asilikaliwa akugwiritsa ntchito mabwato awo apa madzi kupulumutsa anthuwa. Pafupipafupi anthu okwana 6,145 ndi amene akhudzidwa kwambiri ndi madziwa. Malingana ndi chiwerengero chomwe khonsolo ya bomali […]

The post Asilikali apulumutsa nawo anthu ku Dwangwa appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください