Asilamuwo atentha dambwe m’mudzi wa Mchinga kwa mfumu Njombwa ku Kasungu chifukwa gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu kukalowa naye ku dambweko. Malingana ndi wailesi ya Zodiak, gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu kukalowa naye ku dambweko ndipo izi ndi zomwe zinayambitsa mkangano pakati pa magulu awiriwa. A Paul Dickson omwe anaona izi […]
The post Asilamu atentha dambwe ku Kasungu appeared first on Malawi24.