Apolisi pa Jenda akukanika kumanga mwana wa amfumu

Anthu a kwa Inkosi Khosolo ku Mzimba adzudzula apolisi a pa Jenda ponena kuti akulephera kumanga bambo wina yemwe anakwatira mwana wazaka 15. Anthu akuganiza kuti apolisi akukanika kumanga bamboyo popeza ndi mwana wa a Inkosi Khosolo. Nkhaniyi inavumbuluka ndi mabungwe womenyera maufulu a ana m’bomali. Mabungwewo anachita chotheka kukamuchotsako mwanayo kubanjako koma chodabwitsa ndichakuti […]

The post Apolisi pa Jenda akukanika kumanga mwana wa amfumu appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください