Apolisi m’boma la Salima awotcha chamba chochuluka

Apolisi awotcha chamba chokwana matani awiri chomwe akhala akulanda  m’boma la Salima. A Rabecca Ndiwate omwe ndi mneneri wa a polisi m’bomali ati chamba chomwe chatenthedwachi ndi chomwe eni ake adathawa ndipo sakudziwika. Mneneriyu wati apolisi apitiliza kuonetsetsa kuti m’bomali muli chitetezo chokhwima pofuna kuthana ndi mchitidwe wogula komanso kugulitsa mankhwala ozunguza bongo mwachinyengo. A […]

The post Apolisi m’boma la Salima awotcha chamba chochuluka appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください