Malipoti osatsimikizika akusonyesa kuti apolisi munzinda wa Blantyre amanga anthu awiri powaganizira kuti anali nawo mu gulu la anamalira omwe anatchingira nsewu mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera pa mphambano ya HHI ku Blantyre, koma ofalitsa nkhani za apolisi mdziko muno wati atitsimikizirabe ngati mphekeserazi zili zoona. Lachisanu lapitali, kunali […]
The post Apolisi ayamba kumanga omwe anatchingira nsewu Chakwera ku Blantyre appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 
