Nthambi ya apolisi dziko muno yachotsa ntchito apolisi awiri amene amagwira ntchito m’boma la Thyolo chifukwa cha kulephera kusunga mwambo komaso kujomba ku ntchito mopanda chilolezo. Mu kalata yomwe wasainira ndi wachiwiri kwa mkulu wayang’anira antchito ku nthambiyi, Maxton Kalimanjira, ikufotokoza kuti apolisi awiriwa analephera kusunga mwambo komanso amachoka malo ogwirira ntchito mosatsatira malamulo. Malinga […]
The post Apolisi awiri awachotsa ntchito ku Thyolo appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 