Apolisi ati mipingo ili ndi udindo wolangiza akhristu zakuyipa kodzimangilira

Apolisi mu boma la Machinga apempha amipingo kuti pamene akulalikira mau a Mulungu kwa akhristu awo, asamalepherenso kukamba nkhani zokuyipa kwa imfa zobwera chifukwa chodzimangilira komanso kuyipa kwa kulanga okha munthu yemwe akuganiziridwa kuti wapalamula mulandu. Mkulu wapolisi woona zachitetezo cham’madera akumudzi mi boma la Machinga, Sub Inspector Masautso Katemera, ndi yemwe wayankhula izi kumipingo […]

The post Apolisi ati mipingo ili ndi udindo wolangiza akhristu zakuyipa kodzimangilira appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください