Apolisi okwana atatu omwe amagwira ntchito pa police ya Nkhunga m’boma la Nkhotakota, ayimitsidwa ntchito ndi nthambi ya chitetezo ya Malawi Police kamba kokhudzidwa pa nkhani yogulitsa chamba. Kuyimitsidwa ntchitoku kwadza pamene a polisiwa adapezeka okhudzidwa kuti iwo adagulitsa chamba cha makilogalamu ochuluka omwe adalanda kwa mkulu wina m’boma lomwelo. Apolisiwa adamangidwa ndipo akuyankha mulandu […]
The post Apolisi atatu ayimitsidwa ntchito kamba ka chamba appeared first on Malawi 24.