Apolisi ku mu Mzinda Lilongwe anjata anthu asanu ndi anayi (9) powaganizira kuti ndi mbava zomwe zimafuna kuba fetereza ndi chimanga ku kampani ya za ulimi ya Agricultural Research and Extension Trust (ARET). Malingana ndi mneneli wa polisi ku Lilongwe a Hastings Chigalu ati anthuwa ananyamula zida zoopsa kuphatikizapo zikwanje ndi zitsulo zomwe amafuna kukatsekulira […]
The post Apolisi apulumutsa fetereza ndi chimanga ku mbava appeared first on Malawi 24.