Apolisi ku Ndirande mu mzinda wa Blantyre, awombera ndikupha mzibambo wina yemwe akumuganizira kuti amafuna kukaba ku nyumba kwa wachiwiri kwa wamkulu wa apolisi m’chigawo cha ku m’mwera cha ku mzambwe. Malingana ndi ofalitsa nkhani za apolisi m’chigawo cha ku m’mwera cha ku mzambwe, a Joseph Sauka, tsizinamtoleyu wakumana ndi mazangazimewa usiku wa Lolemba pa […]
The post Apolisi apha mbava poyiwombera appeared first on Malawi 24.