Bambo wina wazaka 41 zakubadwa m unzinda wa Lilongwe ku Nsungwi, ali mu ululu mkazi wake atamuthira madzi otentha pamimba ndipo pakadali pano mkaziyu akusungidwa mchitokosi cha apolisi kaamba kochita zaupanduzi. Mkaziyu yemwe dzina lake ndi mayi Promise Kamtepa wazaka 21 zakubadwa adathira madzi otentha dzulo amuna awo a Limbikani Mulota pamimba pamene amuna awo […]
The post Apolisi anjata mayi wina kamba kowotcha mamuna wake ndi madzi otentha appeared first on Malawi 24.