Nzako akati konzu naweso umati konzu. Uwu ndi mwambi omwe makolo a ophunzira pa sukulu ya sekondale ya Karonga Girls agwiritsa ntchito popeleka mphatso ya ng’ombe kwa aphunzitsi kamba kokhozetsa bwino nayeso a JCE komaso MSCE chaka chino. Sukulu ya atsikana ya Karonga inakhozetsa ana onse pa mayeso a Junior Certificate of Education (JCE) chaka […]
The post Aphunzitsi apatsidwa ng’ombe kamba kokhonzetsa bwino ana appeared first on Malawi 24.