Aphunzitsi akuchita zionetsero ku Machinga

Aphunzitsi m’boma la Machinga athamangira ku ofesi ya mkulu wa maphunziro m’bomalo komwe akuti akufuna kupeza mayankho pa ganizo la ofesiyo yokweza ndalama ya welofeya   opanda chidziwitso.  Malingana ndi m’modzi mwa aphunzitsi, yemwe tayankhula naye, yemwe afuna kuti tisawatchule dzina, akuti ofesi ya za maphunziro m’bomali yadula ndalamayi pa malipilo a mwezi wa April, 2024.  […]

The post Aphunzitsi akuchita zionetsero ku Machinga appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください