Aphungu anyumba yamalamulo ati ndi okhonzeka kuthana ndi umphawi wamaphunziro omwe wafika pa 87 perecenti omwe ulipo makamaka msukulu za dziko lino zomwe zikubwezeretsa maphunziro pambuyo. Izi zinanenedwa pamene bungwe lowona nkhani za maphunziro la Civil Society Education Coalition (CSEC) linali ndi nkumano ndi aphunguwa komanso mabungwe mu mzinda waLilongwe omwe amakambirana njira yamakono ya […]
The post Aphungu awonetsa kukhudzika ndi umphawi msukulu za dziko lino appeared first on Malawi 24.