Aphungu avala ziguduli ku nyumba ya malamulo

Kunali chipwilikiti ku nyumba ya malamulo lero pomwe aphungu otsutsa boma anavala mayekete, madilesi ndi mabuluku opangidwa kuchokera ku masaka ati pokwiya ndi ulamuliro wa Lazarus Chakwera. Malingana ndi aphungu ena, iwo anaganiza zovala ziguduluzi ngati njira imodzi yowonetsa kusakondwa kwawo ndi omwe mtsogoleri wa dziko lino a Chakwera akuyendetsera boma ponena kuti zinthu zambiri […]

The post Aphungu avala ziguduli ku nyumba ya malamulo appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください