Apepese! A Malawi akwiya ponenedwa kuti achule

Anthu ochuluka mdziko muno akupitilira kukakamiza nduna yowona za mphamvu ya magetsi a Ibrahim Matola kuti abwere poyera ndikupepesa kaamba konena kuti anthu omwe akudandaula kuti Lazarus Chakwera akuyendayenda kwambiri ndi achule. Mosalingalira kuti kunena kwa ndithe ndithe nanthambwe anazitengera, a  Matola anayankhula izi Lolemba pa 6 June ku Golomoti m’boma la Dedza komwe mtsogoleri […]

The post Apepese! A Malawi akwiya ponenedwa kuti achule appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください

コメントを残す

メールアドレスが公開されることはありません。 が付いている欄は必須項目です