Anyamata oshanganipa pa tauni anjatidwa ku Lilongwe

Makosana awili ku Lilongwe athilidwa zingwe ndi apolisi kamba kowaganizira kuti akhala akubera anthu ponamizira kuti ndi ochita bizimezi yoyendetsa galimoto zonyamula anthu. Nkhani yonse ikuti makosana awiliwa omwe mayina awo ndi a Alick Kazembe azaka 42 zakubadwa komanso a Moses Mponda azaka 35, lamulungu lapitali adanyamula bambo wina pa Roundabout ya MRA nthawi mkuti […]

The post Anyamata oshanganipa pa tauni anjatidwa ku Lilongwe appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください