Anyamata akuthamanga kuposa Kalulu munzinda wa Mzuzu lero

Mpikisano othamanga wa Mzuzu City Half Marathon wayambika pamene ma athletes ayamba kuthamanga mtunda okwana 21 kilometres kuchokera pa St John’s munzinda wa Mzuzu. Kuno kuli liwiro lamtondo wadooka pamene anyamata komanso asungwana akulikumba liwiro kuposa kalulu, inde inu kuli kuthamanga kuposa galimoto. Ma athletes omwe analembetsa mu mpikisano umenewu ndi oposa 130 ndipo kuyelekeza […]

The post Anyamata akuthamanga kuposa Kalulu munzinda wa Mzuzu lero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください