Yemwe akufuna kudzayimira chipani cha Democratic Progressive Party (DPP) m’dera la Chiradzulu Masanjala pa zisankho za 2025 a Rockie Chipenembe, awuza Malawi24 kuti ku dera kwawo anthu akufuna iwowo kuti akhale Phungu, chifukwa ndi wachinyamata komanso ali ndi masophenya zomwe zingathandizile kutukula deralo. Malingana ndi a Chipenembe, kudera kwawo kukupelewela zinthu zambiri komanso anthu ambiri […]
The post Anthu kudera kwathu akufuna mtsogoleri wachinyamata komanso wamasomphenya — atero a Chipenembe appeared first on Malawi 24.
Moni Malawi 