Anthu ku Zomba ati zinthu zikuvuta chifukwa MCP ikufuna kulamula yokha

Anthu ena okhala mu Mzinda wa Zomba ati zinthu mdziko muno zikuvuta kwambiri pankhani ya achinyamata kupeza ntchito, njala komanso kukwera kwa zinthu chifukwa chipani cha MCP chikufuna chidzilamulira chokha osafunanso kumagwiritsa ntchito mfundo zachipani cha UTM. Malinga ndi a Patrick Gremu amene amachita malonda mumzindawu omwe Malawi24 yayankhula nawo, ati chipani cha MCP chidalowa […]

The post Anthu ku Zomba ati zinthu zikuvuta chifukwa MCP ikufuna kulamula yokha appeared first on Malawi24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください