Anthu ku Chiradzulu adandaula ndi mchitidwe wa chinyengo m’ma Admarc

Anthu ena m’boma la Chiradzulu adandaula kuti maofisala a bungwe la Admarc akugulitsa chimanga kwa mavenda mwachinyengo. M’modzi mwa amai pamalopa s Lanesi Liviyeli a mudzi mwa Ching’amba T/A Onga anati ma iwo omwe anati anafika pamalopa 5 koloko ndipo anawona ma ofisalawa akumalowesa mavenda kukhomo lakuseli ndikumatuluka ndi matumba a 25 kilogalamu okwana asanu […]

The post Anthu ku Chiradzulu adandaula ndi mchitidwe wa chinyengo m’ma Admarc appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください