Nduna ya zaumoyo a Khumbize Kandodo Chiponda yapempha mafumu, atsogoleri amipingo komanso achitetezo kuti azidziwitsa achipatala msanga akadziwa kuti pali ena omwe akubisa munthu yemwe ali ndi zizindikiro za kolera. Muchikalata chomwe atulutsa dzulo, a Chiponda ati anthu ena omwe ali ndi zizindikiro za kolera monga kusanza ndikutsekula m’mimba akumakana kupita kuchipatala. Malingana ndi a […]
The post Anthu ena omwe akudwala kolera akumakana kupita kuchipatala – adandaula a zaumoyo appeared first on Malawi24.