Anthu ena dzulo ku Magomero m’boma la Dedza apha mayi oyembekezera ndi mamuna wake ataotcha nyumba yomwe awiriwa amagonamo. Phungu wa delari a Auzious Chidovu watsimikizira wailesi ya Zodiak za nkhaniyi. A Chidovu ati munthu wina adabwereka ndalama kwa banjalo ndipo ndalamayo imamukanika kubweza. Pofuna ndalama zake, bambo amene wamwalirayu anakalanda matumba atatu a chimanga […]
The post Anthu ena apha mayi oyembekezera ndi mamuna wake ku Dedza appeared first on Malawi24.