Nanga inu adzalozerana chiyani mukadzatsamaya? Ndalama osamangodya ngati kuti ndi tomato yemwe mukuopa kuti awola mukakhalitsa naye: anthu uku atutumuka ndi chinyumba cha malemu Goodall Gondwe, ndipo kuli kulozerana kwinaku akuomba m’manja kuti Phuu! Kuli kusavetsetsa ndi zomwe apenya. Anthu ochuluka tchimo lomwe ali nalo ndilosakumbuka kumanga nyumba zokhalamo; osangoti nyumba wamba koma nyumba zomwe […]
The post Anthu ayamba kulozerana nyumba ya malemu Goodall Gondwe appeared first on Malawi24.