Anthu atatu avulala pa ngozi ya pa Salima Turn-off

A Polisi ya Kanengo ati mwana mmodzi ndi akulu-akulu awiri avulala pa ngozi yomwe idachitika dzulo pakati pa galimoto ya mtundu wa Tipper ndi Minibus pa Salima Turn-off ku Lilongwe. Malingana ndi wofalitsa nkhani za polisi ya Kanengo, a Gresham Ngwira, ngoziyi yachitika Galimoto ya Mtundu wa Tipper yi itasempha msewu ndi kuomba minibus yomwe […]

The post Anthu atatu avulala pa ngozi ya pa Salima Turn-off appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください