Anthu atatu apezeka ndi nthenda yofilitsa maso ku Blantyre

Anthu atatu apezeka ndi nthenda yofilitsa maso yomwe muchingerezi imatchedwaconjunctivitis kapena kuti pink eye mu mzinda wa Blantyre. Malingana ndi kalata yomwe atulutsa owona zaumoyo komanso chisamaliro cha anthu m’bomali, ndipo yasainidwa ndi Dr Gift Kawalazira, m’modzi mwa anthuwa wapezeka pa chipatala chaching’ono cha Chilomoni ndipo ena awiri pa chipatala cha Kadidi. Kalatayi yapitiliza kunena […]

The post Anthu atatu apezeka ndi nthenda yofilitsa maso ku Blantyre appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください