Anthu atatu akuganiziridwa kuti adaba malata ku Police College

Bwalo la Senior Resident Magistrate ku Zomba latulutsa pa bail anthu atatu omwe akuganidziridwa kuti adaba malata ku Police College pa 26 November panthawi ya zipolowe zomwe zidabuka pakati pa apolisi ndi anthu okhala mamdera a Chikanda, Mpondabwino, Kazembe ndi Chilupsa pomwe apolisi adaphulitsa utsi okhetsa misozi. Bwaloli lakananso kupereka belo kwa anyamata ena awiri […]

The post Anthu atatu akuganiziridwa kuti adaba malata ku Police College appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください