A Polisi akwa Jenda m’boma la Mzimba amanga anthu atatu atawapeza ndi Chamba mdera la Luviri chomwe amafuna apite nacho ku Lilongwe. Mneneri wa a polisi ya Jenda, Sub Inspector Macfarlen Mseteka, wawuza Malawi24 kuti anthuwa adagwidwa akufufuza mayendwe wopita ku Lilongwe mpomwe anthu adatsina khutu a Polisi mderalo. Womwe apalamula mlanduwu ndi mayi Pilirani […]
The post Anthu atatu agwidwa atapezeka ndi Chamba kwa Jenda ku Mzimba appeared first on Malawi 24.