Anthu asanu ndi mmodzi amwalira, ambiri avulala pa ngozi ya ku By-pass ku Lilongwe

Zachitika ku msewu wa By-Pass ku Lilongwe komwe anthu asanu ndi mmodzi amwalira ndipo ena atatu avulala modetsa nkhawa pangozi ziwiri zomwe zachitikira malo amodzi. Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati Lamulungu, galimoto ya mtundu wa truck ya kampani ya Central Poultry inali itafa, kotero inangoima pa msewu. Cha ma 7 koloko […]

The post Anthu asanu ndi mmodzi amwalira, ambiri avulala pa ngozi ya ku By-pass ku Lilongwe appeared first on Malawi Nyasa Times – News from Malawi about Malawi.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください