Anthu am’mudzi mwa Chimombo awona ngati kutulo atapha njoka 301 lero

Zina ukamva kamba anga mwala, zina zikamachitika nkumati kodi  ndiku Malawi komkuno? Inu anthu am’mudzi mwa Chimombo mdera la mfumu yayikulu Kachere m’boma la Dedza lero pa 12 December ali kukamwa yasa atapha njoka 301 m’munda wina. Nkhani yonse ikuti anthu ena anawona njoka ziwili zikulowa pa dzenje m’mundawo kenako iwo anaganiza zoti akumbe kuti […]

The post Anthu am’mudzi mwa Chimombo awona ngati kutulo atapha njoka 301 lero appeared first on Malawi 24.

マラウイニュースメルマガ登録

メルマガ限定配信のマラウイ超ローカルニュースが無料で受け取れます

マラウイ・アフリカ・国際協力に興味があったら登録しよう!

プライバシーポリシーについてはこちらを確認してください